Yeremiya 52:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mfumu ya Babulo inachititsa khungu Zedekiya+ ndipo kenako inamumanga ndi maunyolo amkuwa n’kupita naye ku Babulo.+ Kumeneko anamuika m’ndende mpaka tsiku la imfa yake. Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 52:11 Yeremiya, ptsa. 158-159
11 Mfumu ya Babulo inachititsa khungu Zedekiya+ ndipo kenako inamumanga ndi maunyolo amkuwa n’kupita naye ku Babulo.+ Kumeneko anamuika m’ndende mpaka tsiku la imfa yake.