Yeremiya 52:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako gulu lonse lankhondo la Akasidi, lomwe linali ndi mkulu wa asilikali olondera mfumu uja, linagwetsa mpanda wonse wa Yerusalemu.+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 52:14 Yeremiya, tsa. 159
14 Kenako gulu lonse lankhondo la Akasidi, lomwe linali ndi mkulu wa asilikali olondera mfumu uja, linagwetsa mpanda wonse wa Yerusalemu.+