Yeremiya 52:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Anthu onyozeka pakati pa Ayudawo, anthu ena onse amene anatsala mumzindamo,+ anthu amene anathawira ku mbali ya mfumu ya Babulo ndi amisiri onse aluso, Nebuzaradani mkulu wa asilikali olondera mfumu, anawatenga kupita nawo ku ukapolo.+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 52:15 Yesaya 2, tsa. 404
15 Anthu onyozeka pakati pa Ayudawo, anthu ena onse amene anatsala mumzindamo,+ anthu amene anathawira ku mbali ya mfumu ya Babulo ndi amisiri onse aluso, Nebuzaradani mkulu wa asilikali olondera mfumu, anawatenga kupita nawo ku ukapolo.+