Yeremiya 52:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 M’chaka cha 23 cha ulamuliro wa Nebukadirezara, Nebuzaradani mkulu wa asilikali olondera mfumu anatenga Ayuda 745 kupita nawo ku ukapolo.+ Anthu onse amene anawatenga anali 4,600.
30 M’chaka cha 23 cha ulamuliro wa Nebukadirezara, Nebuzaradani mkulu wa asilikali olondera mfumu anatenga Ayuda 745 kupita nawo ku ukapolo.+ Anthu onse amene anawatenga anali 4,600.