Maliro 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ziyoni watambasula manja ake.+ Iye alibe womutonthoza.+Yehova walamula onse ozungulira Yakobo kuti akhale adani ake.+Yerusalemu wakhala chinthu chonyansa pakati pawo.+ Maliro Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:17 Nsanja ya Olonda,9/1/1988, tsa. 26
17 Ziyoni watambasula manja ake.+ Iye alibe womutonthoza.+Yehova walamula onse ozungulira Yakobo kuti akhale adani ake.+Yerusalemu wakhala chinthu chonyansa pakati pawo.+