Maliro 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Aneneri ako aona masomphenya achabechabe ndi opanda pake+ onena za iwe.Iwo sanaulule zolakwa zako kuti akuteteze n’cholinga choti usatengedwe kupita ku ukapolo,+Koma anali kuona masomphenya achabechabe ndi osocheretsa+ onena za iwe. Maliro Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:14 Nsanja ya Olonda,9/1/1988, tsa. 26
14 Aneneri ako aona masomphenya achabechabe ndi opanda pake+ onena za iwe.Iwo sanaulule zolakwa zako kuti akuteteze n’cholinga choti usatengedwe kupita ku ukapolo,+Koma anali kuona masomphenya achabechabe ndi osocheretsa+ onena za iwe.