Maliro 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anaziri+ ake anali oyera kuposa chipale chofewa.+ Analinso oyera kuposa mkaka.Ndipotu anali ofiira+ kuposa miyala yamtengo wapatali ya korali. Analinso osalala ngati mwala wa safiro.+
7 Anaziri+ ake anali oyera kuposa chipale chofewa.+ Analinso oyera kuposa mkaka.Ndipotu anali ofiira+ kuposa miyala yamtengo wapatali ya korali. Analinso osalala ngati mwala wa safiro.+