Maliro 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ansembe ndi aneneriwo akungoyendayenda mumsewu ngati anthu akhungu.+ Aipitsidwa ndi magazi,+Moti palibe amene akukhudza zovala zawo.+
14 Ansembe ndi aneneriwo akungoyendayenda mumsewu ngati anthu akhungu.+ Aipitsidwa ndi magazi,+Moti palibe amene akukhudza zovala zawo.+