Ezekieli 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kunsi kwa mapiko anayi a zamoyozo kunali manja a munthu.+ Zamoyozo zinali ndi nkhope ndiponso mapiko.+
8 Kunsi kwa mapiko anayi a zamoyozo kunali manja a munthu.+ Zamoyozo zinali ndi nkhope ndiponso mapiko.+