Ezekieli 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ponena za maonekedwe a nkhope zawo, zamoyo zinayi zimenezi zinali ndi nkhope ya munthu,+ nkhope ya mkango+ mbali ya kumanja,+ nkhope ya ng’ombe yamphongo+ mbali ya kumanzere,+ ndiponso nkhope ya chiwombankhanga.+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:10 Nsanja ya Olonda,3/15/1991, tsa. 99/15/1988, tsa. 11
10 Ponena za maonekedwe a nkhope zawo, zamoyo zinayi zimenezi zinali ndi nkhope ya munthu,+ nkhope ya mkango+ mbali ya kumanja,+ nkhope ya ng’ombe yamphongo+ mbali ya kumanzere,+ ndiponso nkhope ya chiwombankhanga.+