Ezekieli 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Umu ndi mmene nkhope zawo zinalili. Mapiko awo+ anali otambasukira m’mwamba. Chamoyo chilichonse chinali ndi mapiko awiri ogundana, ndipo mapiko ena awiri anali kuphimba matupi awo.+
11 Umu ndi mmene nkhope zawo zinalili. Mapiko awo+ anali otambasukira m’mwamba. Chamoyo chilichonse chinali ndi mapiko awiri ogundana, ndipo mapiko ena awiri anali kuphimba matupi awo.+