Ezekieli 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pamene ndinali kuyang’ana zamoyozo, ndinangoona kuti pansi panali wilo limodzi pafupi ndi zamoyozo,+ pambali pa nkhope zinayi za chamoyo chilichonse.+
15 Pamene ndinali kuyang’ana zamoyozo, ndinangoona kuti pansi panali wilo limodzi pafupi ndi zamoyozo,+ pambali pa nkhope zinayi za chamoyo chilichonse.+