Ezekieli 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Maonekedwe a mawilowo+ anali ngati kuwala kwa mwala wa kulusolito,+ ndipo mawilo anayiwo anali ofanana. Kapangidwe kake kanali ngati kuti wilo lina lili pakati pa wilo linzake.*+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:16 Nsanja ya Olonda,3/15/1991, tsa. 9
16 Maonekedwe a mawilowo+ anali ngati kuwala kwa mwala wa kulusolito,+ ndipo mawilo anayiwo anali ofanana. Kapangidwe kake kanali ngati kuti wilo lina lili pakati pa wilo linzake.*+