Ezekieli 1:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Zamoyozo zikamayenda, mawilowo analinso kuyenda. Zikaima chilili, mawilowonso anali kuima chilili. Zamoyozo zikakwera m’mwamba kuchoka pansi, mawilowonso anali kukwera m’mwamba ali pambali pa zamoyozo, pakuti mzimu wa zamoyozo unali m’mawilowo.+
21 Zamoyozo zikamayenda, mawilowo analinso kuyenda. Zikaima chilili, mawilowonso anali kuima chilili. Zamoyozo zikakwera m’mwamba kuchoka pansi, mawilowonso anali kukwera m’mwamba ali pambali pa zamoyozo, pakuti mzimu wa zamoyozo unali m’mawilowo.+