Ezekieli 5:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndidzakutumizirani njala ndi zilombo zakupha+ ndipo zidzakupherani ana anu. Mliri+ ndi magazi+ zidzadutsa pakati panu ndipo ine ndidzakubweretserani lupanga.+ Ineyo Yehova ndi amene ndanena zimenezi.’” Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:17 Nsanja ya Olonda,10/15/1988, tsa. 11
17 Ndidzakutumizirani njala ndi zilombo zakupha+ ndipo zidzakupherani ana anu. Mliri+ ndi magazi+ zidzadutsa pakati panu ndipo ine ndidzakubweretserani lupanga.+ Ineyo Yehova ndi amene ndanena zimenezi.’”