Ezekieli 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kupansi kwa mapiko a akerubiwo,+ kunaoneka chinachake chokhala ngati dzanja la munthu.