Ezekieli 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 kapena akamapita, mawilo aja anali kupita nawo limodzi ali pambali pawo.+ Akerubiwo akatambasula mapiko awo kuti akhale pamwamba pa dziko lapansi, mawilo sanali kutembenukira kwina, anali kungokhala pambali pa zamoyozo.+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:16 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, tsa. 15
16 kapena akamapita, mawilo aja anali kupita nawo limodzi ali pambali pawo.+ Akerubiwo akatambasula mapiko awo kuti akhale pamwamba pa dziko lapansi, mawilo sanali kutembenukira kwina, anali kungokhala pambali pa zamoyozo.+