Ezekieli 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Uwauze kuti iweyo ndiwe chizindikiro cholosera zam’tsogolo+ kwa iwo. Zidzachitika kwa iwo monga mmene iwe wachitira. Iwo adzapita ku ukapolo, kudziko lina.+
11 “Uwauze kuti iweyo ndiwe chizindikiro cholosera zam’tsogolo+ kwa iwo. Zidzachitika kwa iwo monga mmene iwe wachitira. Iwo adzapita ku ukapolo, kudziko lina.+