Ezekieli 12:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 “Iwe mwana wa munthu, a nyumba ya Isiraeli akunena kuti, ‘Masomphenya amene akuona adzachitika m’tsogolo, ndipo akulosera zinthu zimene zidzachitike m’tsogolo kwambiri.’+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:27 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, tsa. 17
27 “Iwe mwana wa munthu, a nyumba ya Isiraeli akunena kuti, ‘Masomphenya amene akuona adzachitika m’tsogolo, ndipo akulosera zinthu zimene zidzachitike m’tsogolo kwambiri.’+