Ezekieli 16:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Unatenga zovala zako zina n’kupangira malo okwezeka+ okhala ndi mitundu yosiyanasiyana ndipo unayamba kuchitirapo uhule.+ Zoterezi siziyenera kuchitika. Zisamachitike ayi.
16 Unatenga zovala zako zina n’kupangira malo okwezeka+ okhala ndi mitundu yosiyanasiyana ndipo unayamba kuchitirapo uhule.+ Zoterezi siziyenera kuchitika. Zisamachitike ayi.