Ezekieli 19:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako anaukola ndi ngowe n’kuuika m’kakhola ndi kupita nawo kwa mfumu ya Babulo.+ Anapita nawo ataukulunga ndi ukonde wosakira kuti mawu ake asamvekenso m’mapiri a ku Isiraeli.+
9 Kenako anaukola ndi ngowe n’kuuika m’kakhola ndi kupita nawo kwa mfumu ya Babulo.+ Anapita nawo ataukulunga ndi ukonde wosakira kuti mawu ake asamvekenso m’mapiri a ku Isiraeli.+