Ezekieli 38:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Udzabwera pamodzi ndi asilikali a ku Perisiya,+ Itiyopiya+ ndi Puti.+ Onsewa adzanyamula zishango zazing’ono ndipo adzavala zisoti.
5 Udzabwera pamodzi ndi asilikali a ku Perisiya,+ Itiyopiya+ ndi Puti.+ Onsewa adzanyamula zishango zazing’ono ndipo adzavala zisoti.