Ezekieli 38:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “‘Pa tsiku limenelo, tsiku limene Gogi adzabwere m’dziko la Isiraeli, mkwiyo wanga udzatulukira m’mphuno mwanga,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 38:18 Ufumu wa Mulungu Ukulamulira, tsa. 227
18 “‘Pa tsiku limenelo, tsiku limene Gogi adzabwere m’dziko la Isiraeli, mkwiyo wanga udzatulukira m’mphuno mwanga,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.+