Ezekieli 38:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 ‘Ine ndidzalankhula mwaukali wanga+ woyaka moto komanso nditakwiya kwambiri.+ Ndithudi, pa tsikulo m’dziko la Isiraeli mudzachitika chivomezi chachikulu.+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 38:19 Nsanja ya Olonda,10/15/1988, tsa. 17
19 ‘Ine ndidzalankhula mwaukali wanga+ woyaka moto komanso nditakwiya kwambiri.+ Ndithudi, pa tsikulo m’dziko la Isiraeli mudzachitika chivomezi chachikulu.+