Ezekieli 38:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ine ndidzamuweruza+ ndi mliri+ ndiponso magazi.+ Ndidzamugwetsera mvula yamphamvu, matalala,+ moto+ ndi sulufule. Ndidzagwetsa zimenezi pa iyeyo, pagulu lake la asilikali ndi pa mitundu yambiri ya anthu amene adzakhale kumbali yake.+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 38:22 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, tsa. 267/1/1987, tsa. 16 Chisungiko cha Padziko Lonse, ptsa. 155-157
22 Ine ndidzamuweruza+ ndi mliri+ ndiponso magazi.+ Ndidzamugwetsera mvula yamphamvu, matalala,+ moto+ ndi sulufule. Ndidzagwetsa zimenezi pa iyeyo, pagulu lake la asilikali ndi pa mitundu yambiri ya anthu amene adzakhale kumbali yake.+
38:22 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, tsa. 267/1/1987, tsa. 16 Chisungiko cha Padziko Lonse, ptsa. 155-157