Danieli 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 M’chaka chachiwiri cha ufumu wa Nebukadinezara, Nebukadinezarayo analota maloto.+ Malotowo anamuvutitsa maganizo+ ndipo tulo tinamuthera. Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:1 Nsanja ya Olonda,9/1/2007, tsa. 18 Ulosi wa Danieli, ptsa. 46-48
2 M’chaka chachiwiri cha ufumu wa Nebukadinezara, Nebukadinezarayo analota maloto.+ Malotowo anamuvutitsa maganizo+ ndipo tulo tinamuthera.