Danieli 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamenepo Akasidi anayankha mfumu m’chinenero cha Chiaramu+ kuti: “Inu mfumu mukhale ndi moyo mpaka kalekale.*+ Tiuzeni ife atumiki anu zimene mwalota ndipo tikumasulirani malotowo.”+
4 Pamenepo Akasidi anayankha mfumu m’chinenero cha Chiaramu+ kuti: “Inu mfumu mukhale ndi moyo mpaka kalekale.*+ Tiuzeni ife atumiki anu zimene mwalota ndipo tikumasulirani malotowo.”+