Danieli 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti mukapanda kundiuza malotowo, chilango chija+ sichidzakuphonyani. Koma mwagwirizana kuti mundiuze mawu abodza+ kufikira zinthu zitasintha. Choncho ndiuzeni zimene ndalota. Mukatero, ndidziwa kuti mungathe kumasulira malotowo.”
9 Pakuti mukapanda kundiuza malotowo, chilango chija+ sichidzakuphonyani. Koma mwagwirizana kuti mundiuze mawu abodza+ kufikira zinthu zitasintha. Choncho ndiuzeni zimene ndalota. Mukatero, ndidziwa kuti mungathe kumasulira malotowo.”