-
Danieli 2:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Akasidiwo anayankha mfumuyo kuti: “Palibe munthu padziko lapansi amene angathe kuuza inu mfumu zimene mukufuna, pakuti palibe mfumu yaikulu kapena bwanamkubwa amene anauzapo wansembe wochita zamatsenga kapena munthu wolankhula ndi mizimu kapena Mkasidi kuti achite zimenezi.
-