Danieli 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pa nthawi imeneyo Danieli analankhula mwanzeru ndi mozindikira+ kwa Arioki mkulu wa asilikali olondera mfumu, amene anali atanyamuka kale kuti akaphe amuna anzeru a m’Babulo.
14 Pa nthawi imeneyo Danieli analankhula mwanzeru ndi mozindikira+ kwa Arioki mkulu wa asilikali olondera mfumu, amene anali atanyamuka kale kuti akaphe amuna anzeru a m’Babulo.