-
Danieli 2:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Kenako Danieli anabwerera kunyumba kwake ndipo anauza anzake aja, Hananiya, Misayeli ndi Azariya za nkhani imeneyi.
-