Danieli 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Anawauza zimenezi ndi cholinga choti iwo apemphe Mulungu wakumwamba+ kuti awachitire chifundo+ ndi kuwaululira chinsinsi chimenechi,+ kuti Danieli, anzakewo ndi amuna anzeru ena onse a m’Babulo asaphedwe.+
18 Anawauza zimenezi ndi cholinga choti iwo apemphe Mulungu wakumwamba+ kuti awachitire chifundo+ ndi kuwaululira chinsinsi chimenechi,+ kuti Danieli, anzakewo ndi amuna anzeru ena onse a m’Babulo asaphedwe.+