Danieli 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Zitatero, Danieli anapita kwa Arioki,+ amene mfumu inali itamutuma kuti akaphe amuna anzeru a m’Babulo.+ Anapita kwa iye n’kumuuza kuti: “Musaphe mwamuna aliyense wanzeru m’Babulo. Ndipititseni kwa mfumu,+ kuti ndikamasulire maloto ake.”
24 Zitatero, Danieli anapita kwa Arioki,+ amene mfumu inali itamutuma kuti akaphe amuna anzeru a m’Babulo.+ Anapita kwa iye n’kumuuza kuti: “Musaphe mwamuna aliyense wanzeru m’Babulo. Ndipititseni kwa mfumu,+ kuti ndikamasulire maloto ake.”