Danieli 2:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mfumuyo inafunsa Danieli, amene anali kutchedwa kuti Belitesazara,+ kuti: “Kodi ungathe kundiuza maloto amene ndinalota ndi kuwamasulira?”+
26 Mfumuyo inafunsa Danieli, amene anali kutchedwa kuti Belitesazara,+ kuti: “Kodi ungathe kundiuza maloto amene ndinalota ndi kuwamasulira?”+