Danieli 2:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Koma kuli Mulungu kumwamba amene ndi Woulula zinsinsi,+ ndipo wakudziwitsani, inu Mfumu Nebukadinezara, zimene zidzachitike m’masiku otsiriza.+ Maloto anu ndi masomphenya amene munaona muli pabedi lanu ndi awa: Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:28 Ulosi wa Danieli, ptsa. 48-49 Nsanja ya Olonda,11/15/1986, tsa. 6
28 Koma kuli Mulungu kumwamba amene ndi Woulula zinsinsi,+ ndipo wakudziwitsani, inu Mfumu Nebukadinezara, zimene zidzachitike m’masiku otsiriza.+ Maloto anu ndi masomphenya amene munaona muli pabedi lanu ndi awa: