Danieli 2:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Sikuti chinsinsi chimenechi chaululidwa kwa ine chifukwa chakuti ndine wanzeru kuposa munthu wina aliyense ayi,+ koma chaululidwa ndi cholinga chakuti ndikumasulireni malotowo mfumu, ndiponso kuti mudziwe maganizo a mumtima mwanu.+
30 Sikuti chinsinsi chimenechi chaululidwa kwa ine chifukwa chakuti ndine wanzeru kuposa munthu wina aliyense ayi,+ koma chaululidwa ndi cholinga chakuti ndikumasulireni malotowo mfumu, ndiponso kuti mudziwe maganizo a mumtima mwanu.+