Danieli 2:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Mutu wa chifaniziro chimenechi unali wopangidwa ndi golide wabwino,+ chifuwa chake ndi manja ake zinali zasiliva,+ mimba yake ndi ntchafu zake zinali zamkuwa,+
32 Mutu wa chifaniziro chimenechi unali wopangidwa ndi golide wabwino,+ chifuwa chake ndi manja ake zinali zasiliva,+ mimba yake ndi ntchafu zake zinali zamkuwa,+