Danieli 2:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Ndipo Danieli anapempha mfumu kuti iike Sadirake, Mesake ndi Abedinego+ kuti akhale oyang’anira chigawo cha Babulo, ndipo mfumuyo inawaikadi. Koma Danieli anali kutumikira m’nyumba ya mfumu.+
49 Ndipo Danieli anapempha mfumu kuti iike Sadirake, Mesake ndi Abedinego+ kuti akhale oyang’anira chigawo cha Babulo, ndipo mfumuyo inawaikadi. Koma Danieli anali kutumikira m’nyumba ya mfumu.+