Danieli 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tsopano wolengeza mauthenga+ anayamba kufuula kuti: “Tamverani inu anthu a mitundu yosiyanasiyana, olankhula zinenero zosiyanasiyana.+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:4 Ulosi wa Danieli, ptsa. 73-74
4 Tsopano wolengeza mauthenga+ anayamba kufuula kuti: “Tamverani inu anthu a mitundu yosiyanasiyana, olankhula zinenero zosiyanasiyana.+