-
Danieli 3:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Chifukwa cha mawu amenewa, patangomveka kulira kwa lipenga, chitoliro, zeze wamng’ono, zoimbira zosiyanasiyana za zingwe, chitoliro chathumba ndi zipangizo zosiyanasiyana zoimbira, anthu onse a mitundu yosiyanasiyana,+ olankhula zinenero zosiyanasiyana, anagwada mpaka nkhope zawo pansi ndi kulambira fano lagolide limene mfumu Nebukadinezara inaimika.
-