-
Danieli 3:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Koma chifukwa chakuti mfumu inalamula zimenezi itapsa mtima kwambiri ndipo ng’anjo ya moto anaisonkhezera mopitirira muyezo, asilikali amphamvu amene anatenga Sadirake, Mesake ndi Abedinego aja ndi amene anaphedwa ndi malawi a moto.
-