Danieli 3:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndipo amuna ena amphamvuwa, Sadirake, Mesake ndi Abedinego, anagwera pakatikati pa ng’anjo yoyaka moto.+
23 Ndipo amuna ena amphamvuwa, Sadirake, Mesake ndi Abedinego, anagwera pakatikati pa ng’anjo yoyaka moto.+