Danieli 3:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pamenepo, mfumu Nebukadinezara anachita mantha kwambiri ndipo ananyamuka mwachangu. Iye anauza nduna zake zapamwamba kuti: “Kodi sitinaponye amuna atatu amphamvu pakati pa moto titawamanga?”+ Ndunazo zinamuyankha kuti: “Inde, mfumu.”
24 Pamenepo, mfumu Nebukadinezara anachita mantha kwambiri ndipo ananyamuka mwachangu. Iye anauza nduna zake zapamwamba kuti: “Kodi sitinaponye amuna atatu amphamvu pakati pa moto titawamanga?”+ Ndunazo zinamuyankha kuti: “Inde, mfumu.”