Danieli 3:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndiyeno mfumu inati: “Taonani! Inetu ndikuona amuna amphamvu anayi akuyendayenda pakati pa moto osapsa, ndipo munthu wachinayiyo akuoneka ngati mulungu.”+
25 Ndiyeno mfumu inati: “Taonani! Inetu ndikuona amuna amphamvu anayi akuyendayenda pakati pa moto osapsa, ndipo munthu wachinayiyo akuoneka ngati mulungu.”+