Danieli 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Zizindikiro zake n’zazikulu ndipo zodabwitsa zake n’zamphamvu.+ Ufumu wake udzakhalapo mpaka kalekale+ ndipo ulamuliro wake udzakhalapo ku mibadwomibadwo.+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:3 Ulosi wa Danieli, ptsa. 82-84 Mtendere Weniweni, ptsa. 70-71
3 Zizindikiro zake n’zazikulu ndipo zodabwitsa zake n’zamphamvu.+ Ufumu wake udzakhalapo mpaka kalekale+ ndipo ulamuliro wake udzakhalapo ku mibadwomibadwo.+