Danieli 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako Danieli, amene ndinamupatsa dzina lakuti Belitesazara+ pofuna kulemekeza mulungu wanga,+ amenenso mwa iye muli mzimu wa milungu yoyera,+ anabwera kwa ine ndipo ndinamuuza malotowo. Ndinati: Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:8 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),10/2016, tsa. 14 Ulosi wa Danieli, ptsa. 84-85
8 Kenako Danieli, amene ndinamupatsa dzina lakuti Belitesazara+ pofuna kulemekeza mulungu wanga,+ amenenso mwa iye muli mzimu wa milungu yoyera,+ anabwera kwa ine ndipo ndinamuuza malotowo. Ndinati: