Danieli 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “‘Iwe Belitesazara mkulu wa ansembe ochita zamatsenga,+ ndikudziwa bwino kuti mzimu wa milungu yoyera uli mwa iwe+ ndipo palibe chinsinsi chimene umavutika nacho.+ Chotero ndiuze zimene ndinaona m’maloto anga ndi kumasulira kwake.+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:9 Nsanja ya Olonda,9/1/2007, tsa. 18
9 “‘Iwe Belitesazara mkulu wa ansembe ochita zamatsenga,+ ndikudziwa bwino kuti mzimu wa milungu yoyera uli mwa iwe+ ndipo palibe chinsinsi chimene umavutika nacho.+ Chotero ndiuze zimene ndinaona m’maloto anga ndi kumasulira kwake.+