Danieli 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “‘Nditagona pabedi langa, ndinapitiriza kuona masomphenya ndipo ndinangoona mlonda+ woyera+ akutsika kuchokera kumwamba. Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:13 Ulosi wa Danieli, ptsa. 85-86
13 “‘Nditagona pabedi langa, ndinapitiriza kuona masomphenya ndipo ndinangoona mlonda+ woyera+ akutsika kuchokera kumwamba.