Danieli 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mlondayo anali kulankhula mofuula kuti: “Gwetsani mtengowo+ ndipo dulani nthambi zake. Yoyolani masamba ake ndi kumwaza zipatso zake. Nyama zithawe pansi pake ndipo mbalame zichoke panthambi zake,+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:14 Kukhala ndi Moyo Kosatha, ptsa. 138-140 Mtendere Weniweni, ptsa. 71-72
14 Mlondayo anali kulankhula mofuula kuti: “Gwetsani mtengowo+ ndipo dulani nthambi zake. Yoyolani masamba ake ndi kumwaza zipatso zake. Nyama zithawe pansi pake ndipo mbalame zichoke panthambi zake,+