Danieli 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 koma musiye chitsa chake munthaka. Chitsacho muchikulunge ndi mkombero wachitsulo ndi wamkuwa. Chikhale pakati pa udzu wakutchire ndipo chizinyowa ndi mame akumwamba. Chikhalenso pakati pa nyama zakutchire ndi udzu wa padziko lapansi.+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:15 Ulosi wa Danieli, ptsa. 85-86, 90-92 Mtendere Weniweni, ptsa. 71-72
15 koma musiye chitsa chake munthaka. Chitsacho muchikulunge ndi mkombero wachitsulo ndi wamkuwa. Chikhale pakati pa udzu wakutchire ndipo chizinyowa ndi mame akumwamba. Chikhalenso pakati pa nyama zakutchire ndi udzu wa padziko lapansi.+